
Yesu Khristu, pogwira mawu a Malaki kwa Anefi
Taonani, ndidzakutumizirani Eliya mneneri, lisadadze tsiku lalikulu ndi loopsa la Ambuye; Ndipo adzatembenuza mitima ya atate kwa ana, ndi mitima ya ana kwa atate awo, kuopa kuti ndingadze ndi kukantha dziko lapansi ndi thembelero.
Mpulumutsi woukitsidwa akubwereza lonjezo la Malaki lokhudza Eliya kwa anthu a ku Amerika, kuonetsa kufunika kwake.